Thread
While waiting, he asked me a question
"Kodi Esther, kwanu anakukonza?"
"Ndati, anakukonzani kwanu"
"Mukutanthauza kuti agogo ako anangololela kuti uyambe ntchito osakukonza? Olo mphini imodzi sanakutemele?"
I said "No" and man looked at me like I had just said the earth was flat
"Ukutanthauza kuti ukamabwera kuntchito kuno, umasamba madzi a waterboard basi?"
Me: "Pali madzi enanso oti ndizisamba?"
Now even I was shocked
So I'm like, "Pali waterboard yina yoti madzi ake amalemeletsa"
I was shocked again, "Anthu amalandila ndalama zina kuposa salary yawo"
Mr M "Eya"
Me:
So I asked "Inuyo moti munazikonza mulipa"
He goes "Ukatoyesa"
In a slow tone I said "Inu ozikonza mukandipemphe ine osamba madzi a waterboard ine, kapempheni okozedwa anzanu"
Anyway, have a beautiful lunch. Men, remember to talk about your problems, the suicide rates are scary. Wouldn't want to lose you.
Stay blessed honies